\v 13 Pamene Mulungu ananilengesa kucoka pa nyumba ya batate banga na kuyenda kucoka ku malo aba kupita pa malo pena. Ninakamba kuti kwa eve, ' ufanika unilangize kukhulupilika kwako monga mkazi wanga: Pamalo paliponse pamene tizayenda, ukambe za ine, " Ninabadwa naye." \v 14 Ndipo Ambimeleki anatenga mbelele na ng'ombe, na akapolo bamuna na bakazi, na kubapeleka kwa Abrahamu. Ndipo anambwezela Sara, mkazi wa Abrahamu, kwa eve.