Rubeni, ndiwe mwana wanga oyamba, mpamvu yanga, na kuyamba kwa mpamvu yanga, ulemu opambana na mpamvu yopambana. Osauzika monga manzi oyenda na mpamvu suzapambana, chifukwa unakwela pa bedi ya batate bako.