\v 3 Anati, "Ambuye banga, ngati napeza mwai mumenso mwanu, napapata musapitilire wanchito wanu." \v 4 Lekani manzi yang'ono yabwekesewe, sambani kumendo, pumulani pansi pa mtengo. \v 5 Lekani nibwelese cakudya cing'ono, kuti muzipumulise imwe mweka. Kucoka apo mungayende, pakuti mwabwelela kwa wanchito wanu. " Bananyankha." Cita monga mwamene wakambila.