\v 18 Kuli Enoki kuna badwa Iradi. Iradi anankhala tate wa Mehujeli. Mehujeli anakhala tate wa Methusheli. Methusheli anankhala tate wa Lamekhi. \v 19 Lamekhi ana kwatila ba kadzi babili. zina yamukadzi umodzi inali Ada, na zina yamukadzi wina inali Zilla.