\v 17 Ndipo Abrahamu anapemphela kwa Mulungu, ndipo Mulungu anapolesa Abimeleki, mkazi wake, na bakapolo bake bakazi kuti bakwanise kunkhale na bana. \v 18 Pakuti Yehova analengesa onse bakazi ba mnyumba mwa Abimeleki bankhaliletu osabala, cifukwa ca Sara, mkazi wa Abrahamu.