\v 18 Pamene Yakobo anacoka kufumila ku padamu Aramu, anafika bwino ku mzinda wa Shekemu, malo yopezeka mu Kenani anaphumulila pafupi ndi mzinda. \v 19 Ndipo anagula malo pamene anamangila Hema kucokela ku mwana wa Hamo, tate wa Shekemu, ndi mutengo wa Hundriredi ziduswa za siliva. \v 20 Kuja anamanga guwa ndikuipatsa zina kuti Eli Elone Isilayeli.