\c 43 \v 1 Njala inapitila mu malo. \v 2 zinacitika pamene bana diya chakudya zamene bana bwelesa ku Igipito, ba tate babo bana kamba ku libeve, "Endani futi, tigulani vakudya."