\v 9 Mukulu opeleka chakumwa anamu uza chiloto chake Yosefe. Anamu uza kuti, onani, mutengo unali pasongolo panga. \v 10 Mumutengo munali ntambi zitatu. Pamene unapulika, maluba anachoka ndipo unabala mpesa zakupya. \v 11 Chiko cha Farao chinali mumanja mwanga. Ninatenga mpesa nakuzi fyantila mu chiko cha Farao, ndipo ninaika chiko mumanja mwa Farao."