Thu Sep 30 2021 12:23:12 GMT+0200 (Central Africa Time)
This commit is contained in:
parent
83d39a9a94
commit
78d219511d
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 22 \v 23 \v 24 Nditayang'ana m'loto langa, tawona, ngala zisanu ndi ziwiri zinamera pa phesi limodzi, zodzala ndi zabwino. Ndipo tawona, ngala zina zisanu ndi ziwiri, zofota, zopyapyala, zopsereza ndi mphepo ya kum'mawa, zinamera pambuyo pawo. Ngala zowondazo zinameza ngala zisanu ndi ziwiri zabwinozo. Ndidawauza amatsenga aja, koma panalibe wondimasulira ine. "
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 25 \v 26 Yosefe anati kwa Farao, "Maloto a Farao ndi ofanana. Chimene Mulungu akufuna kuchita watiuza kwa Farao. Ng'ombe zisanu ndi ziwiri zabwinozo ndi zaka zisanu ndi ziwiri, ndipo mitu isanu ndi iwiri yabwino ndi zaka zisanu ndi ziwiri. Malotowo ndi ofanana.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 27 \v 28 \v 29 Ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziŵiri zoonda ndi zosakondeka zimene zinatuluka pambuyo pawo ndizo zaka zisanu ndi ziŵiri, ndiponso ngala zisanu ndi ziŵiri zoonda zotenthedwa ndi mphepo ya kum'maŵa zidzakhala zaka zisanu ndi ziŵiri za njala. Ichi ndi chinthu chomwe ndidalankhula ndi Farao. Zomwe Mulungu akufuna kuchita wamuululira Farao. Taonani, zaka zisanu ndi ziwiri zakuchuluka kwakuchuluka zidzadza m'dziko lonse la Aigupto.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Zaka zisanu ndi ziwiri za njala zidzafika pambuyo pawo, ndipo zochuluka zonse zidzaiwalika m'dziko la Aigupto; ndipo njalayo idzaononga dziko. Zochulukazo sizidzakumbukiridwa mdziko chifukwa cha njala yomwe idzatsatire, chifukwa idzakhala yoopsa kwambiri. Kuti malotowo abwerezedwa kwa Farao ndichifukwa choti nkhaniyi yakhazikitsidwa ndi Mulungu, ndipo Mulungu achita posachedwa.
|
Loading…
Reference in New Issue