Wed Nov 25 2020 15:05:08 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2020-11-25 15:05:09 +02:00
parent d17143b7b4
commit 6f3fad06bc
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 16 \v 17 Yudah anakamba, "Tingakambe chani kwa bwana wanga? Tizakamba chani? Kodi tingazilungamitse bwanji? Muungu aipYosefe anakamba, "Chinkale patali naine cha mutundu uyu kuti ninga chichite, Munthu wamene enze apezeka na kape m'kwanja mwake, uyu munthu anzankala kapolo wanga, koma kwa imwe benangu mutende mwa mtendele kwa atate anu." Kuchoka apo Yudah ababwela pafupi naye nakukamba, "'Mfumu yanga, anapapata lekani wanchito wanu akambeko ku munthu yanu, ndipo mu saleke ukali wanu kuti uyonekele pali kapolo wanu. Chifukwa imwe ni chimodzi modzi na Falao.
\v 16 \v 17 Yudah anakamba, "Tingakambe chani kwa bwana wanga? Tizakamba chani? Kodi tingazilungamitse bwanji? Muungu aipeza chimo ya mbadwa mubanchito banu. Ona, ndife bakapolo ba bwana wanga, Ise nawamene kapu yopezeka mumanja mwake. Yosefe anakamba, "Chinkale patali naine cha mutundu uyu kuti ninga chichite, Munthu wamene enze apezeka na kape m'kwanja mwake, uyu munthu anzankala kapolo wanga, koma kwa imwe benangu mutende mwa mtendele kwa atate anu." Kuchoka apo Yudah ababwela pafupi naye nakukamba, "'Mfumu yanga, anapapata lekani wanchito wanu akambeko ku munthu yanu, ndipo mu saleke ukali wanu kuti uyonekele pali kapolo wanu. Chifukwa imwe ni chimodzi modzi na Falao.