Thu Sep 30 2021 12:27:12 GMT+0200 (Central Africa Time)
This commit is contained in:
parent
998ae588e9
commit
5fd153b99a
|
@ -0,0 +1 @@
|
||||||
|
\v 39 \v 40 \v 41 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, "Popeza Mulungu wakuwonetsa iwe izi zonse, palibe wina wakuzindikira ndi wanzeru ngati iwe. Iwe ukhala woyang'anira nyumba yanga, ndipo monga mwa mawu ako anthu anga onse adzalamulidwa. kukhala wamkulu kuposa iwe. " Farao anati kwa Yosefe, "Taona, ndakukhazika iwe woyang'anira dziko lonse la Aigupto."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
||||||
|
\v 42 \v 43 Farao anavula mphete yake yosindikizira mdzanja lake naiveka pa dzanja la Yosefe. Anamuvekanso zovala za nsalu yabwino kwambiri, ndipo anam'manga ndi tcheni chagolide m'khosi mwake. Anamuyendetsa m'galimoto yachiwiri yomwe anali nayo. Amuna adafuwula patsogolo pake, "Gwadani bondo." Farao anamuika kukhala woyang allanira dziko lonse la Igupto.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
||||||
|
\v 44 \v 45 Farao anati kwa Yosefe, "Ine ndine Farao, ndipo kupatula iwe, palibe munthu amene adzatambasule dzanja lake kapena phazi lake m landdziko lonse la Igupto." Farao anatcha dzina la Yosefe "Zafenati-Panea." Anamupatsa Asenati, mwana wamkazi wa Potifera wansembe wa Oni, kuti akhale mkazi wake. Yosefe anayenda m thedziko la Igupto.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
||||||
|
\v 46 \v 47 Yosefe anali wa zaka makumi atatu pamene anaimirira pamaso pa Farao, mfumu ya Aigupto. Ndipo Yosefe anatuluka pamaso pa Farao, napitapita pa dziko lonse la Aigupto. M'zaka zisanu ndi ziwiri zochuluka dzikolo linabereka zochuluka.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
||||||
|
\v 48 \v 49 He gathered up all the food of the seven years that was in the land of Egypt and put the food in the cities. He put into each city the food from the fields that surrounded it. Joseph stored up grain like the sand of the sea, so much that he stopped counting, because it was beyond counting.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
||||||
|
Joseph had two sons before the years of famine came, whom Asenath, the daughter of Potiphera priest of On, bore to him. 51Joseph called the name of his firstborn Manasseh, for he said, "God has made me forget all my trouble and all my father's household." 52He called the name of the second son Ephraim, for he said, "God has made me fruitful in the land of my affliction."
|
Loading…
Reference in New Issue