Sun Nov 22 2020 10:23:55 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Bshop2 2020-11-22 10:23:57 +02:00
parent 1976af53f5
commit 4f7dd9f0b9
124 changed files with 124 additions and 0 deletions

1
01/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 1 \v 1 Po yamba, Mulungu anapanga ku mwamba na ziko ya pansi. \v 2 Ziko inalibe maonekedwe yabwino ndipo yenzelibe vinthu vilivonse. Mudima unali pamwamba pa nyanja. Muzimu wa Mulungu unali kuyenda pamwamba pa manzi.

1
01/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Mulungu nakamba, "lekani kuwale," ndipo kunawala. \v 4 Mulungu anaona kuti kuwala kunali bwino. Anapatula kuwala kucoka ku mudima. \v 5 Mulungu anapasa zina ya kuwala "muzuba," na mudima "usiku." Kwenze kumazulo na kuseni, siku yoyamba.

1
01/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Mulungu anakamba, "Lekhani pa nkhale kupatuka kwa manzi, ndipo lekani manzi ya patukane ku chokela ku manzi. \v 7 Mulungu anapanga mulenga lenga no patula manzi yanali pansi pa mulenga lenga na pa mwamba pa mulenga lenga. china nkhala mwamena. \v 8 Mulungu ana itana mulenga lenga " Mu mwamba." Iyi mumazulo na kuseni, siku ya chiwili.

1
01/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Mulungu anakamba, "Lekhani manzi pansi yakhale pa malo yomozi, lekhani malo yo yuma ya aneke," Chi na nkhale mwamene. \v 10 Mulungu ana itena malo yo yuma "ziko." na yonse manzi anaitana "nyanja." anaona ati inali yabwino.

1
01/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Mulingu anakamba, "lekani ziko ichose vomela: mitenfgo yo bala mbue ndi cipaso mutengo obala cipaso camene mbeu ili mukati, ili yonse yopalana na mutundu wake." chi nkhala mwamene. \v 12 Ziko ina chosa vomela, vomela vochosa mbeu yolingana na mutundu wake. mitengo yo bala cipaso yolingana na mutundu wake. Mulungfu anaona kuti zinali bwino. \v 13 Apa kunli kuma zolu na kuseni. siku yoyamba.

1
01/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Mulungu anakamba," lekani munkale vo sanika mwamba kuti ku patule usiku na muzuba ndipo vinkale vo uneselako, nyengo, masiku na zaka. \v 15 Lekani vo sanika vili mu mwanba vipase ku wala ziko. Chinali mwamene.

1
01/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Mulungu anapanga zo sanikila vili vikulu, Ikulu imozi ku lamulila muzuba, ndi ing,ono ku lamulila usiku. Anapanga anso nenyezi. \v 17 Mulyngu anaviyika mu mwamba kuti vizi pasa ku wala pa ziko, \v 18 ku lamulia muzuba ndi usiku, ndi ku patula ku wala kuli mudima. Mulungu anaona ati inli ya bwino. \v 19 Ndiye ku nali ku mazulo ndipo kuseni. siku ya nambala fo

1
01/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Muliungu anakamba,"lejani manzi ya zule na zo lengewa za moyo za mbili, ndi nyoni zo mbululuka pa mwamba pa pa ziko mu mulenga lenga". \v 21 Mulungu ana lenga vo lengewa vikulu vamu nyanja, na vonse vili na moyo mwatundu wake, lengewe vamene vima yenda ndi zo zulisa manzi konse, ndi zi nyoni zonse zama papiko mwamutundu wake. Mulungu anaona arti inLI BWINO.

1
01/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Mulungu ana zidalisa, ku kamba kuti nkalani "balanani ndipo mupake," ndipo ku zulisa manzi yamu nyanja. Lekani nyoni zi pake pa ziko. \v 23 Kunali ku mazulo ndipo kuseni.Siku ya faive

1
01/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Mulungu anakamba,"Lekani ziko iyi chose zo lengewa za moyo, ili yonse ku lingana na mutundu wake, zobeta, vinthu vokwaba, ndipo ni nyama vapa ziko ya pansi, ili yonse ku lingana na mutundu wake". Chinali mwamene. \v 25 Mulungu anapanga vi nyama vonse ku lingN na mutndu wake ndipo vonsew vonse vokwaba pa ntaka na mutundu wake. Anaona ati chili bwino.

1
01/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 Mulungu anakamba,"Lekani ti pange munthu muchi fanizo chatu, muma onekedwe yatu. Lekani ankale na ulamulili pali nsomba zamu nyanja, na pali nyoni zamu mwamba, na zobeta, na zonse zapa ziko ya pansi na vonse vokwaba pa ziko ya pansi. (malembedwe yena ya kalke yali ndi "pa mwamba pa zobeta, pa mwamba pa nyama zapa ziko ya pansi ndipo vonse vo kwaba pa ziko ya pansi") \v 27 Mulungu anakenga munthu mu chi fanizo chake. Mu chi fanizo cjake anamu lenga iye. Mwamuba na Mukazi anaba lenga iye.

1
01/28.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 28 Mulungu anaba dalisa ndiku pba uza "Balanani, mupakaise. zulisani ziko ya pansi ndiku gonjesa. Nkalani na ulamulilo pali nsomba zamu nyanja, pali nyoni za mulenga lenga, ndipo vonse vinthu va moyo vamene viyencda pa ziko ya pansi". \v 29 Mulungu anakamba," Ona, naku pasa vomela vopasa mbeu ili pa ziko, na mutengo ulina chipaso chili na mbeu mukati mwake. viza nankala vo kudya vako.

1
01/30.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 30 Ku chinyama chili chonse pa ziko ya pansi, nyoni za ku mwamba, na vonse vo lengewe vili na mpepo ya moyo. Napasa vomela vonse kuti vinkale vokudya". Chi na nkala mwamene. \v 31 Mulungu anaona vonse vamene anapanga. Onani, chi nali bwino maningi. Ndiye kunali kumazulo na kuseni, siku ya nambala sikisi

1
01/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 1

1
06/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 6 \v 1 Zinacitika izi pamene anthu anayamba kupaka pa ziko lonse na bana banakazi anabadwa kwa iwo. \v 2 Bana amuna a mulungu anaona bana banakazi ba anthu kuwama. Ndipo anabakwatira kunkhala akaazi awo aliyense anasankhapo wake. \v 3 Yahova anati, " Mzimu wanga suzapitiliza kulimbana na munthu nthawi yonse, cifukwa iye ali munthu. Moyo wake azakala zaka izo."

1
06/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Vimbinga vinali pa calo pa masiku yaja, ndi pambuyo pake. Izi zinacitika pamene bana ba muna ba mulungu anakwatila bana ba kazi ba anthu ndipo bana balilana bana. Amena anali vimbinga panthawi ija ya kale ndi zomveka.

1
06/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Yawe anaona kuti kuyipa mtima kwa munthhu kuli kukula pa ziko, ndipo maganizo yao ya mitima yao yanali yoipilathu nthawi zonse. \v 6 Yahova cinamubaba kuti anapanga munthu pa ziko, ndipo anamvela kuipa mumutima wake.

1
06/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Ndipo Yehova ananena, " Nizacosapo mtundu wa anthu wamene ndina mpanga ine pa calo ca pansi - mtundu wa anthu ndi nyama, ndi zokalaba zonse ndi tunyoni twamwamba, cifukwa nimvela kuipa kuti ninampanga izi." \v 8 Koma Nowah anapeza mwayi pamaso pa Yehova.

1
06/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Izi ndiye zamena zinacitika kwa Nowah. Nowah analiye munthu wolungama, ndipo pakati pa anthu analibe ili yonse pa nthuwi yake. \v 10 Nowa annayenda na Mulungu. Nowa anakhalatate wa bana bamuna batatu: Shemu, Hamu ndi Jafeti.

1
06/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Ziko linaipa pa meso ya Mulungu ndipo inali yozula na ciwawa. \v 12 Mulungu danaona ziko; Onani, Inali yoipa kwamnbili cifukwa muntu aliyense woipa mujila yonse ya ziko.

1
06/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Mulungu anakamba na Nowa, " Naona kuti yakwana nthuwi, kuti nicosepo munthu wonnse cifukwa calo cazola na ciwawa vicitika mwa iye, Zoonadi, Nizabaononga pamozi ndi ziko. \v 14 Koma kuli iwe upange chombo kucokela kuci mtengo ca kipulesi. Upange zipinda mu chombo ndi kuyanzikapo coletsa manzi kungena mkati na kunja. \v 15 Umu ndiye mwamena uzapangila: Kutalimpa kwa chombo ikale mikonoila 300, kufupika kwake mikono ili 50, ndikutalimpa mikono 30.

1
06/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Upange mtenge wa chombo ndi usilize ndi mkono umodzi kuyambila pa mwamba pa cipuna. Uyikipo ciseko kumbali kwa chombo ndipo upange capansi, cacibili ndi cacitatiu cogonapo. \v 17 Nvela nili pafupi nakubwelesa cigumula ca manzi yambili pa ziko, kuonanga vintu vonse vamoyo va pa ziko. vonse pa ziko vizamwalila.

1
06/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Koma nizanga chipangano na iwe uzabwela mu chombo, iwe na bana bako bamuna, na mukazi wako, na bakazi ba bana bako bamuna. \v 19 Ndi zolengendwa zonse zamoyo zibili zibili uzibwelese mu chombo, zimuna na zikazi, zinkale na umoyo na iwe.

1
06/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Vinyoni kulingana na mtundu wake, pa nyama kulingana ndi mtundu wake, pa zokalaba za pa dothi kulingana ndi mtundu wake, zibili zosi yana zizabwela kuli iwe kuzisunga namoyo. \v 21 ika pamozi vakudya vosiyala ndipo usunge kuti vikhale vakudya na vao." \v 22 Ndipo Nowa anacita izi. Kulingana na vonse vamena Mulungu anamulamulila, ndipo anacita.

1
06/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 6

1
07/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 7 \v 1 Yehova ana kamba kuli Nowa, "Bwela, iwe mzonse zamunyumba mwako, mu combo, diponso naoka kutindiwe ulungama pamanso panga mu mbado uwu. \v 2 Pa nyama zonse zo tela utele zi muna zili seveni ndi zikazi zili seveni pa nyama zosa yela, pali izo ulete zibili imunz ndi ikazi yake. \v 3 Ndi nyoninso zamulengalenga ulete zimuna zili seveni kazi zili seveni kuti mutundu wake usasite oa ziko lonse.

1
07/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Muma siku yali seveni niza lezalengesa nvula ikaloke na ziko kwa ma siku fote ndi usiku fote nizaonanga zonse zamoyo zamane nina panga.'' \v 5 Nowa ana cita vonse vemene Yehova ana mula mulila.

1
07/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Nowa anali na zaka zobadwa sikisi handredi pamene nvula ina loka paziko ya pansi. \v 7 Nowa, bana bake bamuna, mukazi wake, na bakazi ba bana bake bana nge mu combo chifukwa ca nvula.

1
07/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Nyama zo yela na zo sa yela, nyoni na vonse vo kwaba pa ntaka. \v 9 Zibili zibili, imuna naikazi, zina bwela kuli Nowa nongena muchombo, mwamene Mulungu analamulila Nowa. \v 10 Ku coka muma siku wali seveni manzi ya mbili yana bwela pa ziko ya pansi.

1
07/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Mu caka chamene Nowa anali na zaka sikisi handredi mu mwezi wa cibili pa siku ya seventini, pa siku yamene iyi, tusime tonse twa manzi tuna seguka, ndi mazunila aku mwamba yana seguka. \v 12 Nvula ina yamba ku loka ndi kugwa oa ziko ya pansi masiku yali fote zunba ndi usiku.

1
07/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Pasiku yamene iya Nowa bana bake mbamuna, Shemu, Hamu ndi Jafeti namukazi wa Nowa ndi bakazi ba bana ba Nowa banangena mu Chomba. \v 14 Bana ngena pamozi ndi nyama zamu sanga kulingana ndi mutundu wake, ndi zonse zo beta, kulinga na ndi mutundu wake, ndi zokwaba kulinga ndi mutundu wake, ndi nyoni zonse kulingana ndi mutundu wake ndi zina zolengedwa na mapipippo.

1
07/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Vibili vibili vitengedwe vonse va mpweya moyovina kuli Nowa naku ngena mu Chombo. \v 16 Nyama zamene zina ngena zanali zimuna nazikazi zotengdwa zonse; zina ngena moonga Mulungu ana mu lamulila. Ndipo yehova anaba valila ci seko.

1
07/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Ndipo manzi yambili yana bwela pa ziko ya pansi masiku fote, ndipo manzi yana paka naku nyamula chomba cina nyamuka pa mwamba pa ziko. \v 18 Manzi yana zula pamalo yonse ya pa ziko ya pansi naku nyamula chomba pamwamba pa manzi.

1
07/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Manzi yana nyamula maningi pa ziko ya pansi ndipo malupili yonse yanali pansi palenga lenga yana vininkiliwa. \v 20 Manzi yana nyamuka mikono fifitini pamwamba pamapili.

1
07/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Vose vamoyo vinali kuyenda pa ziko ya pansi viana mwalila nyoni, zibeto, nyama zamu sanga, na vonse vo lengedwa va moyo vinali vambili pa ziko ko yonse, ndipo na bantu bonse. \v 22 Vonse vamoyo bolengedwa vamoyo vinali kunkala pansi venzo pema mpweya yamoyo kupitila mu mpuno zaba, zina pa.

1
07/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Ndiponso zonse zamoyo zenze pa ziko zina cosewapo, banthu ndi nyama ndi zokwa ndi nyoni zamlengalenga. Zonse zina onengedwa kucoka pa ziko ya pansi Nowa cabe na banja benze naeve mu chomba bana siyiwa. \v 24 Manzi yanankala pa ziko masiku 150.

1
07/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 7

1
08/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 8

1
11/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 11 \v 1 Ndipo ndziko lonse lapansi ina sebanzesa chilankulindwe chimozi ndipo banali namau yamozi. \v 2 Pamane benzeli kuyenda yenda ku mawa, bana peza malo ku shina ndipo banankala kwamene.

1
11/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Banakambisana, "Bwelani, tapange naku shoka bwino mchelwa." Banali na nchelwa mu malo mwa myala na manenekela ngati ndaka. \v 4 Bana kamba, Bwelani tiyeni tizipangile teka muzinda na nsanja yamene izafika kumwamba, ndipo tizipangile zina ife teka. Naati sitizachita, tizapasulidwa mudziko lonse lapansi.

1
11/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 ndipo Yehova anaseluka pansi kuti aone muzinda na nsanja vamene bana ba adamu banamanga. \v 6 Yehova anakamba, ''onani, nibanthu bamodzi nachikambidwe chimodzi ndipo bayamba kuchita ivi! manji manji kulibe chizankala chovuta kuchita pali vamene baganiza kuchota. \v 7 Bwelani tiyende pansi nakusokoneza chilankulidwe chao, kuti basanvelane,"

1
11/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Ndipo Yehova anaba mwandza- mwandwa kuchoka kuja mu ziko lonse yapansi ndipo banaleka mumanga muzinda. \v 9 Cifukwa chaichi, ziko yaka inali Babelo ku chofukwa kuja Yehova anasokoneza chilankulidwe cha ziko yonse lapansi ndipo kuchokela kuja Yehova anaba mwazamwaza pa ziko lonse.

1
11/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Aba banali bana ba Shemu. Shemu anali nazaka handredi, ndipo anankala tate wa Arphaxad zaka zibili pamene ciina pita chigumula. \v 11 Shemu anankala zaka 500 Pamene anankala tate wa Arphaxad. Anankala futi tate wabana bamuna nabana bakazi benangu.

1
11/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Pamene Arphaxadi anali zaka 35 anankala tate wa Shela. \v 13 Arphaxadi ananakala zaka 403 pamene anankala tate wa shela. Anankala futi tate wa bana bamuna na bakazi benangu.

1
11/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Pamene shela anali na zaka 30 anankala tate wa Eberi. \v 15 Shela anankala zaka 403 pamene anankala tate wa Eberi. Anankala futi tate wabana bena bamuna na bakazi.

1
11/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Pamene Eberi anali na zaka 34, anankala tate wa Pelegi. \v 17 Eberi anali na zaka 430 pamene anankala tate wa Pelegi. Anankala futi tate wabana bamuna na bakazi benangu.

1
11/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Pamene Pelegi anali na zaka 30 anankala tate wa Reu. \v 19 Pelegi anankala zaka 209 pamene anankala tate wa Reu. Anankla futi tate wabana bamuna na bakazi.

1
11/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Pamene Reu anali na zaka 32 anankala tate wa Serugi. \v 21 Reu anankala zaka 207 pamene anankla tate wa Serugi. Anankala futi tate wabana bamuna na bakazi benangu.

1
11/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Pamene Serugi anali na zaka 30 anannkala tate wa Naholi. \v 23 Serugi anakala zaka 100 pamene anankala tate wa Nahori. Anankala futi tate wabana bamuna na bakazi benangu.

1
11/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Pamene Nahori anali na zaka 39 anankala tate wa Tera. \v 25 Nahori anankala zaka 119 pamene anankala tate wa Tera. Anankala futi Tate wa ban bamuna n a bakazi benangu. \v 26 Pamene Tera anali na zaka 70, anankala tate wa Abrahamu, Nahori na Harani.

1
11/27.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 27 Ndipo aba banli bana ba Tela. Tela anankala tate wa Abrahamu, Nahori, na Harani ndipo Horani anankala tate wa Loti. \v 28 Harani anafela pa pamenso ya Tela tate wake muziko yamene anabadwilamo ku Uri mu Kalidea.

1
11/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Abrahamu na Nahoro bana tenga bakazi. Zina yamukazi wa Nahoro inali Milika, mwana wa Harani, wamene enzeli tate wa Milika na Isaki. \v 30 Ndipo Sarai anali mkazi wamene senzekubala; anali mwana.

1
11/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 Tela ana tenga Abramu mwamuna wa mwana wake mwamuna Harani, na Sarai mupongozi wake, mukazi wamwana wake mwamuna abranu, ndipo pamozi bana choka mu Uri waku Kalidea, kuyenda ku Harani ya Kenani. Koma bana bwela ku Harani ndipo banankala kwamene. \v 32 Tela anankala zaka 205 ndipo anafela mu Harani.

1
11/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 11

1
15/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 15 \v 1 kuchoka ivi vinthu mau ya Yehova yana bwela kwa abulam m'masomphenya, kukamba, "Usa yope, Abramu! ndine wokuchingilila ndipo ndine mphoto yako yaikulu." \v 2 Abramu anakamba kuti, "Ambuye Yehova, muzanipasa chani, pakuti nilibe mwana, ndipo oloba nyumba yanga ni Elyeza waku Damasicus?" \v 3 Abramu anakamba kuti, "Pakuti simunanipase mwana, onani, umozi obadwa munyumba yanga azankhala oni loba!"

1
15/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Ndipo, onani, mau ya mulungu yana bwela kuli eve, kukamba, "Uyo munthu saza nkhala oloba waku; koma wamene azachokela kuthupi yako ndiye wamene azankhala oloba wako." \v 5 Ndipo anamubwelelsa panja, na kukamba, "Yangana kumwamba, na kupenda nyenyezi, ngati unga kwanise kuzipenda." Ndipo namuuza kuti, "Ndiye mwamene obadwa mwaiwe bazankhalila."

1
15/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Anakhulupilila Yehova, ndipo chinapendeka kuli eve monga chilungamo. \v 7 Anamuuza iye kute, "Ndine Yehova, wamene anakuchosa mu Uri wa Achaudini, kukupasa malo aya kuti ulobe." \v 8 Anakamba, "Ambuye Yehova, nizaziba bwanji kuti chizankhala choloba changa?"

1
15/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Ndipo anamuuza kuti, "Niletele ng'ombe ikazi yazaka zitatu, mbuzi ikazi yazaka zitatu, nambelele yazaka zitatu, nkhunda, nanjiba. \v 10 anamulete zonse, ndiku yang'amba pa bili, ndiku vifaka vi langanana, coma sana patulisane nyoni. \v 11 pamene vi nyoni vinabwela pansi pama tupi ya nyama yokufa. Abramu ana vi pisha.

1
15/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Ndipo pamene zuba inali kuyenda pansi, Abramu anagona tulo ndipo, onani, vonse vi nali pafupi naye vinakhala mudima ndiku yofya. \v 13 Ndipo Yehova anati kwa Abramu,"ziba kuti bobadwa pa mboyo pako bazankhala alendo pa malo yamene si ili yabo, ndipo banhkala mukapolo ndi ovutisiwa.

1
15/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Nizaweluza calo chija camene bazasebenzela, ndipo kuchoka apo baza choka na vinthu vambili. \v 15 coma muzayenda ku malo yaba tate banu mu mutendere, ndipo muzashikiwa zaka za bwino zaunkhalamba. \v 16 mubadwo wa nambala fo baza bwela futi, po peza machimo yama Amoni yakalibe kufika pama lile,".

1
15/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 \v 18 \v 19 \v 20 \v 21 Pamene zuba inangena ndipo kwenze mudima, onani, poto yenze na chusi ndi nyali yo yaka pakati kama duswa

1
18/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 18 \v 1 Yehova anaonekela kwa Abraham pa mtengo wa Mamre, pamene anankhala pa ciseko pa kazuba ka siku. \v 2 Anayanga kumwamba ndipo, onani anaona bamuna batatu baimilila pasogolo pake. Pamene anabaona, anathamanga kukumana noa kucoka pongenela pa nyumba na kugwanda kuika mu wake pansi.

1
18/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Anati, "Ambuye banga, ngati napeza mwai mumenso mwanu, napapata musapitilire wanchito wanu." \v 4 Lekani manzi yang'ono yabwekesewe, sambani kumendo, pumulani pansi pa mtengo. \v 5 Lekani nibwelese cakudya cing'ono, kuti muzipumulise imwe mweka. Kucoka apo mungayende, pakuti mwabwelela kwa wanchito wanu. " Bananyankha." Cita monga mwamene wakambila.

1
18/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 \v 7 \v 8 Ndipo Abrahamu Anayenda kuli Sara

1
18/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Genesis 18

1
19/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 19 \v 1 Ba ngelo banabwela ku Sodom kumazulo, pamene Loti enzenkale pongenela mu muzinda wa Sodom. Pamene Loti anabawona, ananya mukka kuyenda kubatumanya , anangwada no paka mutu wake pansi. \v 2 Anakamba kuti, " Napapata bakulu banchito yanga, niku pempani kuti mubwele kuny' umba kwa wa chitowanu, munkale usiku, musambe naku meendo. Munganya muke kuseeni noyenda njila yanu." Bana yaanta, " Iyayi, tizagona pano pangila." \v 3 Anapapata cho koselela, banayenda na yeve nongena munyumba. Anakoza zokudya nopanga mukate ulibbe vopakisa, ndipo banadya.

1
19/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 pe bakalibe kogona, bamuna ba mumuzida, bamuna bamu Sodomu, bana zinguluka nyumba bana nabakulu bamuna boonse bamumizinda yonse. \v 5 Bana yitana Loti, banati kuli yeve, " balikuti bamuna bamene babwela kuli iwe usiku uno? balete kuli ise, tibazibe."

1
19/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Ndipo Loti ananyenda panja pachiseko no vala chiseko kumbuyo kwake. \v 7 Akamba, " Namimpempani abbale banga, musachite zo chimwa. \v 8 wayonani, nilina bana bakazi babili bekakalibe kuziba mwamuna. nivomeleseni, niku papatani, kuti nibalete kuli imwe, ndipo muzachita zo kondwelesa aba, chifukwa bamu chinvili chamutenge wanga."

1
19/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Banati, "bwelela mumbuyo! "Bana kamba nafuti, "uyu anabwela kunkala wachilendo, manje afina kunkala woweluza wata! Manje tizamuchita zoyipa kuchila beve." Banalimbana naye mwa muna, banalimbana na Loti, ndipo bana bwela pafupi kufuna kupwanya chiseko.

1
19/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Ndipo bamuna banachosa kwanja no donsele Loti munyumba kuli beeve no vala chiseko. \v 11 Balendo ba Loti bna vela menso ya bamuna benze panja pa chiseko cha myumba, bana na ba kulu, ndipo banalema pe benzo josa kusakila chiseko.

1
19/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Bamuna banakamba kuli Loti. "uliko nawuliwonse pano? Mupongozi mwamuna, mwna mwamuna, mukazi na uliwonse wako mumuzinda, bachose pano. \v 13 Tifuna kuwononga malo ano, chifukwa kulila kwawo kwavenka mamingi kuli yehova ndipo atituma kuti tiwononge malo ano."

1
19/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Loti anayenda kukamba na azipongizi bake bamuna, bamuna bana lonjeza kukwala bana bake, anati, musanga, chokani pamalo aya, chifukwa Yehova afuna kuwononga muzinda."Kubapongozi bake bamuna chinawoneka monga a seka. \v 15 Pamene kunacha, angelo anawuza Loti, kuti, "yambani kuyenda, tenga mukazi wako na bana bako bakazi bali pano, musanyekele pamozi na chilango chamuzinda."

1
19/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Anawayawaya. Ndipo bamuna bangwila kwanya kwake, kwanga kwamukazi wake, namanja yabana bake bakazi kuchoka mumuzinda. \v 17 Pebanabachoza panja, mwamuna umonzi anati, "Tamangilani umoyo wani! musayangene kumbuyo, usankale mumalo yalibe kantu kalikonse. Tamangila kulupili kuti musa nyeke."

1
19/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Loti anati kuli Beeve, "iyaye, napapata, bakulu banchito yanga! \v 19 Wanchito wanu apeza chisomo pamenso yanu, anso mwanilangisa chifundo chopitilila mukupulumusa umoyo wanga. Ndipo siningtamangile kulupili, chifukwa chiwonongeko chachikulu chinganipeze, ndipo nizafa. \v 20 Wona, uja muzinda alipafupi maningi kutabilako, anso nikang'ono napapata, lekani niyenda (sikangono?), Ndipo umoyo wanga uzapulumuka.

1
19/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Anamuwuzu iye, "Chabwino, Nivomekeza pempo iyo, siniza wononga muzinda ye wakamba. \v 22 Yendesa! tanamanga kja, sinizachita chilichose paka ufikeko." Ndipo uyu muzinda unali zowa.

1
19/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Pamene zuba inekwele pa ziko Loti anali anafika ku Zowa. \v 24 Yehova analokesa nvula ya Saufa mu mulilo kuchokela kumwamba mu sodom na Gomora. \v 25 Ana wononga mizinda zija, an malo yalibe kantu kalikoonse , nazonse zamoyo zinanili mumuzinda, nazonse zomela pansi.

1
19/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 Ndipo mukazi wa Loti, anali kumbuyo kwake, anayangana kumbuyo, ana sanduka cuulu cha saulti. \v 27 Abrahamu ananyamuka kuseni, no yenda pa malo pamene enze anayimilila ana Yehova. \v 28 Anayanga pansi ku Sodoma na Gomora nowona, chusi chinyamuka kuchioka pansi monga chusi chamu fanasi.

1
19/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Pomwe Mulungu ana wonnga muzinda wa maloyalibe chilichonse, Abrahamu anabwela mumaganizo ya Mulungu. Anatuma Loti kuchoka pakati pa chiwonengeko pamene anaeononga muzinda wamene Loti analikunkalamo.

1
19/30.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 30 Koma Loti anachoka mu Zowa kuyenda kunkala kupili nabana bake babili bakazi, chifukwa anali na manta kunkala mu Zowa. Anankhala mu cimubo ca mulipili. Eve na bana bake bakazi.

1
19/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 Mwana woyamba anawuza mufana wake, "batate bakakota, kulibe bamuna konse kulibe mwamuna azagona naise monga mweba machitila pa ziko la pansi. \v 32 Bwele, tiye timwese batate moba, ndipo tizagona nabo, kuti tusunge mbewu ya batate batu." \v 33 Uja usiku banapasa batate bawo moba. Ndiponso woyambila anayenda nongona nabatate bake; batate bake sibanazibe pe anagona, na pe anawuka.

1
19/34.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 34 Siku yokonkapo woyambila anawuka mung'ono, "nvela, nonangona nabatate usiku wapita, Tiye tibamwese moba lelo usiku nafuti, ndipo uzayenda kugona nabo, kuti tisunge mbwe yabatate batu." \v 35 Uja usiku nawo banapasa batate bawo moba, ndipo mung'ono anayenda kugona nabatate bawo. Batate bake sibanazibe pe anagona na pe anawuka.

1
19/36.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 36 Bana bonse babili ba Loti banankala na mimba yabatate bawo. \v 37 Woyambbila anabala mwamuna, ndipo anamupasa zina Mohabu. Anankala kolo wana Mobaiti balelo. \v 38 Ndipo mupana wake, anabala mwana mwamuna, no mupasa zina la Ben-ammi-nchipo anankala kolo wa mantu ba Ammoni ba lelo.

1
19/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 19

1
21/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 21 \v 1 Yahova anaikako nzelu kuli Sara monga mwamene ana kambila, na Yahova anachitila Sara vamene ana kamba. \v 2 Sara ana nkhala na mimba nakubala mwana mwamuna wa Abrahamu mu ukhalamba wake pa nthuwi yamene Mulungu ana kamba. \v 3 Abrahamu anamu pasa zina mwana wamene kuli eve, wamene Sara anamu balila, Isaki. \v 4 Abrahamu anamu duka mwana wake Isaki pamene ana kwanisa masiku eiti, monga mwamene Mulungu ana lamulila kuli eve.

1
21/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Abrahamu anali ana zaka handiladi pamene mwana wake Isaki anabandwa. \v 6 Sara anati, " Mulungu ani lengesa ku seka; bonse banza nvela baza seka naine." Ni ndani ana ganizila kuti. \v 7 Ndiposo Sara anati, " Ni ndani ana ganizila kuti Sara anga nkale na bana koma namu balila mwana mwamuna mubu nkalamba wake.

1
21/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Mwana ana kula nakuleka ku nyonkha ndipo Abrahmu ana panda chikondwelelo chacikulu pamene ana siya ku nyoka Isaki. \v 9 Sara ana ona mwana wa Haga waku Egipito, wamene ana balila Abrahamu amuseka.

1
21/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Tsopano anati kuli Abrahamu, " Mu choseni pano kapolo na mwana wake, chifukwa mwana wa kapolo saza nkala oloba pamodzi na mwana wanga Isaki." \v 11 Ichi chinamu nkalila chomu vitisa abrahamu chifukwa cha mwna wake.

1
21/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Ndipo Mulungu anati kuli Abrahamu, " Osa nkala ovutisiwa chifukwa cha mwana, na kapolo wako. Nvele mau yake yonse yamene akamba pali iyi nkani, chigukwa ni muli Isaki mwamene bonse bodwa bakupaza pasiwa zina. \v 13 Ndipo niza pangaso mwana wa kapolo mukazi ziko, chifukwa nobo badwa wako.

1
21/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Ndipo Abrahamu anacita kuseni, naku tenga mukate na chikumba cho tengelamo manzi, naku pasa Haga no ika mwana pamusana pake. Ana yenda ku chipululu ku Bereseba. \v 15 Pamene manzi yanasila muchi kumba cho tengamo manzi, anasiya mwna munsi mwa mtengo. \v 16 Ana yenda, ankala patali na mwana, mutunda wa Muvi, anazi kambisa eka, nisaoneko kufa kwa mwana wanga, "' Ndipo ana nkalapo oneka naye, ana bwela ayamba kulilamo kuwa.

1
21/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Mulungu anamvela kulila kwa mwana, ndipo mungeli wa Mulungu anaitana kuli Haga ku chokela ku mwamba, naku kamba kuli eve, "Ni chani chaku vuta, Haga? Osa yopa chifukwa Mulungu anamvela kulila kwa mwana kwamene alili. \v 18 Nyamuka imika mwana nakumulibisa: chifukwa Nizampanga eve kunkhala ziko ikulu.

1
21/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Ndipo Mulungu anamu segula menso, nakuona chisime cha manzi. Ana yenda nakuika manzi muchi tumba cha manzi, no pasa mwana kumwa. \v 20 Ndipo Mulungu anali mwana uja, ndipo ana kula. Ana nkala mu chipululu Nunkhala wopaya nyama. \v 21 Ana nkala mu chipululu cha Parana, ndipo amai bako anamu tengela mukazi waku malo ya Egipito.

1
21/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Ina fika ntawi pamene Abimeleki na Fikolakulu ankonda ana kamba kuli Abrahamu kuti, "Mulungu ali na iwe mu vonse vamene uchita. \v 23 Tsopano vomele na ine pa Mulungu kuti suza chita boza na ine, olo bana banga nangu bonse bo badwa kuli ine. Ni langize malo yemene unali ku nkalamo monga wachilendo mubu bwino chimozi mozi. \v 24 Abrahamu anati, "Na vomela."

1
21/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Abrahamu ana dandaula pali chisime chamene anamupoka kuli anchito ba Abimeleki. \v 26 Abimeleki anati, " Siniziba wamene ana chita ivo. Koma futi sunai uzepo; panka apa manje." \v 27 Ndipo Abrahamu ana tenga mbelele na ng'ombe naku pasa Abimeleki, na amuna abili naku panga chi pangano.

1
21/28.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 28 Tsopano Abrahamu ana tenga bana ba mbelele seveni zikazi naku zi ika [a zeka. \v 29 Abimeleki anati kuli Abrahmu, " Tantauzo ya izi nyama zamene wa ika pa zeka ni chiyani? \v 30 Ana yankha tenga mu manja mwanga zizani nkalila umboni, kuli nina kumba chisime."

1
21/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 Ndipo malo aya anaya ita beresheba, chifukwa bonse babili bana panga lonjezo. \v 32 Ana panga ma panyano pa Beresheba, na Abimeleki na Fikol, mukulu wa nkonda, ana bwelela ku malo ya filisiti.

1
21/33.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 33 Abrahamu ana shanga chi mtengo cha tamariski ku Beresheba. Napamene apo ana pempeza Yahova, wamuyayaya Mulungu. \v 34 Abrahamu ana nkala wachi lendo mu malo ya Filisiti masiku yambili.

1
21/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 6

1
26/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 26 \v 1 Ndipo kunali mu ziko, kumbali kwanjala yoyamba yamene ina chitikka muma siku ya Abrahamu. Isaki anayenda kuli Abimeleki, mfumu yaba Aphistini ku Gela.

1
26/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Manje Yehova anaonekela kuli eve naku muuza kuti, "usayende ku Egypito; nkala mu ziko yamene nakuuza kunkala. \v 3 Nkala mwamene muno mu zika. Ndipo niza nkala naiwe naku kudalisa iwe; kuli iwe naku bobadwa muli iwe, nizakupasa ma ano chamene ninalapila kuli Abrahamu tate wako.

1
26/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Nizapakisa bobadwa mwa iwe monga nyenyezi za kumwamba, ndipo nizapasa kuli bobabdwa mwa iwe maziko yonse ayakupitila muli iwe maziko yonse ytapansi yazadalisika. \v 5 Nizachita ichi chifukwa Abrahamu ananvelele mau yanga nakusunga malangizo yanga, lamulo langa, malemba yanga, na malamulo yanga."

Some files were not shown because too many files have changed in this diff Show More