Merge branch 'master' of C:\Users\WABW-030\AppData\Local\BTT-Writer\temp\nya-x-nyanja_gen_text_reg[1]\nya-x-nyanja_gen_text_reg into master

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2020-11-26 10:42:55 +02:00
commit 1cbd6f6eaa
73 changed files with 145 additions and 2 deletions

1
08/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 8 \v 1 Mulungu anaganizila pali nowa, vonse vinyama vamu sanga, na vonse vinyama vo beta pa nyumba ve anali navo mu chombo. Mulungu anapanga mpempo kufuzikila pa chalo, na manzi yana yamba kuyamba kungena pansi. \v 2 Tumigodi twa manzi yapatali namazenela yaku mwamba yana valika na mvula inaleka kuloka. \v 3 Manzi yachigumula yana yamba ku ngena pansi pan'gono pan'gono kuchoka pa chalo, ndipo pambuyo pa masiku iso. Manzi yana ngena pansi.

1
08/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Chombo chinankazikika papili la Arareti, mu mwenzi wa seveni siku la seveni. \v 5 Manzi yanapitiliza kungena pansi kufikila mu mwenzi wateni pa siku yo yamba ya mwenzi,myamba ya mulupi inayamba kuonekala.

1
08/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Pamene panapita masiku foti Nowa anasegula zenela yaku chomba chamene anapanga. \v 7 Nakutuma chikwalala chamene chenze mbululuka kuyenda nakubwela futi mpaka kufikila pamene manzi yanayumila pa chalo.

1
08/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Nowa futi anatuma ka nkunda kuti ka kaone ngati manzi yasilila pachalo, \v 9 koma ka nkunda kana soba po ika mendo yake, naku bwelela kuli eve mu chombo. Nowa anachosa kwanja yake, nakuka tenga, nakuka ngenesa mu chombo.

1
08/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Anayembekezako masiku seveni yenangu nakutuma futi ka nkunda ku choka mu chombo. \v 11 Ka nkunda kana bwelela kuli eve mu mazulo. Ona! kukamwa kwake kunali tepo yosayuma ya mpesa yotuolewa manse manse. Mwaicho Nowa anaziba kuti manzi pa ziko ya pansi yana ngena pansi. \v 12 Anayembekezako masiku seveni nakutuma futi ka nkunda, koma sikana bwelele kuli eve futi.

1
08/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Zinali zinachitika mu chaka cha six dundred na chaka cho yamba, mu mwenzi oyamba, pasiku yo yamba yo mu mwenzi, pamene manzi yana yuma mu ziko yapansi. Nowa anasegula cho valila chapa chombo, naku yangana panja, anaona kuti, onani pamwamba pa pansi panze po yuma. \v 14 Mumwezi wachibili, pasiku ya 27 ya mwenzi, ziko yapansi inali yo yuma.

1
08/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Mulungu anati kuli Nowa,, \v 16 "Choka muchombo, ie, mukazi wako, bana bako bamuna, na bakazi bana bako bamene uli nabo. \v 17 Choka na vonse vamoyo vamene uli navo, vinyoni, vinyama, na vonse vamene vimakalaba pa ziko ya pansi kuti vipake maningi pa ziko yanpasi vika balane naku paka pa ziko yapansi."

1
08/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Ndipo Nowa anachoka muchombo na bana bake bamuna, mukazi wake, na bakazi ba bana bake. \v 19 Na vilengedwe vonse vamoyo, vonse vokalaba pansi, na vinyoni, vonse vo yenda pa ziko yapansi kulingana na mabanja yao, yina choka muchombo.

1
08/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Nowa anapanga guwa po pempelela Yehova. anatenga vinyama voyela, na vinyoni voyela naku vipeleka monga nsembe pa guwa yo pempele lapo Yehova. \v 21 Mulungu ana nunsha kafungo ka bwino naku kamba mu mutima wake, "Siniza ka tembelela ntaka futi chifukwa cha bantu, nangu maganizo yamitima yao niyo impa kuyambila ku umwana. Olo kuononga vonse va moyo, monga mwamene na chitila. \v 22 Pamene ziko yapansi ikaliko, ntau yambeu naku kolola kuzizila na kupya, ntau yakupya na ntawi yaku zilila, muzuba na usiku silvzakasiya.

1
08/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 8

1
27/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 27 \v 1 Pamene Isaki anakula na menso yake yanaleka kuonesesa kuti analeka nakuona, anaitana Esau, mwana wake mwamuna mukulu naku mu uza, "Mwana wanga." Esau anati kuli eve "Nili Pano," \v 2 ndipo Isaki anakamba, "Ona kuna nakota siniziba siku yamene nizafa.

1
27/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Chifukwa chaicho tenga zida zako, chola chako cha mivwi, na uta wako, na kuyenda mu sanga nakunigwilila nyama. \v 4 Nipangile chakudya cha bwino, chamene nikonda, ndipo ulete kuli ine kuti nichidye na kuku dalisa iwe nikalibe kufa."

1
27/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Ndipo Rabeka anamvela pamene Iski anali ku kamba na Esau mwana wake. Esu anayenda mu sanga kuti agwile nyama nakuleta. \v 6 Rabeka ana uza Yakobo mwana wake mwamuna kuti, "Yangana kuno, namvela atate bako bakamba na mubale waiko Esau. Bakamba kuti, \v 7 'Niletele nyama yamusanga ndipo unipangile chakudya chabwino, kuti nichidye naku kudatisa iwe pamenso ya Yehova nikalibe kufa.'

1
27/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Ndipo chifukwa chaicho, mwana wanga, mvela mau yanga yamene niku lamula iwe. \v 9 Yenda kuvibeto nakuniletela tubana tw mbuzi tubili twa bwino; ndipo nizatupanga chakudya chabwino cha atate bako, monga mwamene bachikondela. \v 10 Uzapeleka kuli atate bako, kuti bachidye nakukudalisa bakalibe kufa."

1
27/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Yakobo anauza Rabeka amai bake, " Onani, Esau mubale wanga ali na upipi, koma ine ndine mwamuna osalala, \v 12 kapena batate banga baza ni gwila ine, ndipo nizaoneka kuli beve ngati onama. Nizaziletela tembelelo neka osati daliso."

1
27/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Amai bake bana mu uza eve, "Mwana wanga, leka tembelelo ibwele pali ine. Mvelela mau yanga, ndipo yenda, ulete kuli ine." \v 14 Ndipo Yakobo anaenda nakutenga tu bana twa mbuzi tubili naku tuleta kuli bamai bake, ndipo bamai bake bana panga chakudya chabwino, monga atate bake banali ku kondela.

1
27/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Rabeka anatenga vovala va bwino va Esau, mwana wake mukulu mwamuna, wamene anali navo munyumba, naku valika Yakobo, mwana wake mungono mwamuna. \v 16 Ana muvalika chikumba cha ka mbuzi kangono ku manja yake na ku mbali yaku mukosi wake osalala. \v 17 Anaika chakudya cha bwino na mukate wamene anapanga mu manja mwa mwana wake mwamuna Yakobo.

1
27/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Yakobo anaenda kuli ba tate bake naku kamba, "Batate banga." Batate bake bana kamba "Nili pano; ndiwe ndani mwana wanga?" \v 19 Yakobo ana bauza batate bake, "ndine Esau mwana wanu oyamba. Nachita monga mwenze mwani uzila. Manje ukani nakudyako nyama yanga yamusanga, kutimunidalisa ine."

1
27/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Isaki ana mu uza mwana wake mwamuna, "Nanga wanga?" anati, "Chifukwa Yehova Mulungu wanu aileta kuli ine." \v 21 Isaki anati kuli Yakobo, "Bwela pafupi, pali ine kuti nikugwile iwe, mwana waga mwamuna, kuti nizibe gati zo ona ndiwe mwana wanga Esau olo kapena sindiwe."

1
27/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Yakobo anayenda kuli Isaki tate wake, ndipo Isaki anamugwila naku kamba, "Mau ni mau ya Yakobo koma manja ni manja ya Esau. \v 23 Isaki sana muzibe, chifukwa manja yake yenze na upipi, monga ya mubale wake Esau, ndipo Isaki ana mudalisa.

1
27/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Anakamba "Nanga ndiwe zo ona mwana wanga mwamuna Esau?" Anayanka, "Ndiwe" \v 25 Isaki anti "Leta chakudya kuli ine ndipo nizadya nyama yako yamu sanga, kuti nikudalisa." Yakobo ana muletela chakudya: Isaki anadya, Yakoba anamuletela vinyu, ndipo anamwa.

1
27/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 Ndipo atate bake ba isaki bana mu uza. "Manje bwela pafupi nakuni pyopyona mwan wanga mwamuna." \v 27 yakobo anabwela pafupi naku mupyopyona, ndipo ananusha kafungo ka vovala vake na kumudalisa anakamba "Ona, kafungo kam mwana wanga kali monga kamusanga mwamene Yehova ana dalisa.

1
27/28.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 28 Mulungu akapase mbali ya mame yako mwamba, mbali yakuina kwa ziko yapansi, na mbeu zambili na vinyu vanyowani.

1
27/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Lekabantu baku sebenzele na maziko yakugwadile unkale bwana kuli ba bale bako, ndipo leka bana bamai bako bamuna baka gwadile iwe uyo wamene azaku tembelela atembelelewe: Wamene azakudalisa adalisiwe."

1
27/30.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 30 Pamene panja Isaki anasiliza kudalisa yakobo, na yakobo anachoka namata pamenso pa Isaki tate wake Esau mubale wake anabwela kuchokela mukugwila nyama. \v 31 Na eve anapanga chakudya chabwino nakuleta kuli batate bakee. Ana bauza batate bake, " Atate, ukani ndipo mudyeko nyama yamasanga ya mwana wanu,kuti mini dalise."

1
27/32.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 32 Isaki tate wake anakamba kuli eve, "ndiwe ndani?" anati, "Ndine mwana wanu mwamuna oyamba , Esau." \v 33 Isaki ananjenjema maningi nakukamba ati, "Nanga ni ndani wamene enze apaya nyama yamusanga nakuniletela? Ninali nadya yonse ukalibe kubwela, ndipo namudalisa uyo. Zo ona, uyu azankala odalisika."

1
27/34.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 34 Pamene Esau anamvela mau ya atate bake, analila maningi, mokalipa naku kamba kuti kuli batate bake, " Nidaliseni ine, naine batate banga." \v 35 Isaki anakamba, "Mubale wako enze abwela kuno monamiza, nakutenga madaliso yako."

1
27/36.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 36 Esau anakamba, "Uyu zoona zina yake si yakobo chifukwa aninama ine kabili anaipoka choyenela chaku badwa kwanga, ndipo, onani, manje atenga madaliso yanga. Ndipo anakamba, "Simunanisugileko daliso?" \v 37 Isaki anayaka naku kamba kuli Esau, "Ona, namupanga bwana wako, nakumupasa babale bake bonse monga ba nchito, ndipo na mupasa mbeu na vinyu ya sopano. Nanga nichani chamene ningakuchitila, mwana wanga mwamuna?"

1
27/38.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 38 Esau anakamba kuli batate bake, "Mulibe olo daliso imozi yanga, atate banga? Ni daliseni, naine, atate banga." Esau analila mo punda.

1
27/39.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 39 Isaki atate bake banayanka nakukamba kuli eve, "Ona, malo kwamene uzayenda kunkala yaza nkala ku tali na chuma cha ziko yapansi kutali na mame yakumwamba. \v 40 Kupitila mulupanga yako uzankala, naku sebenzela mubale wako. Koma ngati wamu ukila, uzachosa goli yake mu mukosi wako."

1
27/41.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 41 Esau anamuzonda yakobo chifukwa cha madaliso yamene bana mupasa batate bake. Esau anakamba mumutima wake, "Masiku yolila batate banga yali pafupi; yakapita nizamupaya mubale wanga Yakobo." \v 42 Mau ya Esu mwana mwamuna yana uziwa kuli Labeka. Ndipo anaitana Yakobo mwana wake mwamuna mungono naku kamba kuli eve, "Ona Esau azitontoza eka pali iwe pakuganiza ku kupaya iwe.

1
27/43.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 43 Manje, mwana wanga mwamuna, nimvelele ine nakutabila kuli Labani, mubale wanga, mu Halani, \v 44 Kankaleko na eve pangono, mpaka ukali wa mubale wako uchepeko, \v 45 mpaka ukali wamubale wako uchokeko kuli iwe, nakuibala vamene una chita kuli eve. Ndipo nizatuma nakuku bweza kuno. Nichifukwa cha chani niza kutayani bonse babili pa siku imozi?

1
27/46.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 46 Rabeka anakamba kuli Isaki, "Nalema nao umoyo chifukwa cha bana bakazi baku Heti ngati yakobo akwatila bana bakazi bena bana bakazi bakuno kumalo, umoyo wanga uzankala bwino bwnji?"

1
27/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 27

View File

@ -1 +1 @@
\c 31 \v 1 \v 2 \v 3 Ndipo Yakobo anamwa mau ya bana ba Labani, yamene banakamba, " Yakobo atenga vonse va batate bathu, apeza chuma chonse ici kucokela mu vinthu va batate. banthu, apeza
\c 31 \v 1 Ndipo Yakobo anamwa mau ya bana ba Labani, yamene banakamba, " Yakobo atenga vonse va batate bathu, apeza chuma chonse ici kucokela mu vinthu va batate. banthu, apeza chuma conse ici kucokela mu vinthu va batate. \v 2 Yakobo anaona kuyang'anidwe pa menso pa Labani. Anaona kayang'anidwe wake kanacinja. \v 3 Ndipo Yehova anakamba kuli yakobo, " bwelera kuziko ya batate bako na ba bale bako, ndipo nizankhala naiwe.

1
31/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Yacobo anatuma ndipo kuitana Rakele ndi Leya kuti abwere kumundu kuli zobeta zake. \v 5 Ndipo anakamba nabeve. "Naona kayanganidwe kaba tate banu pali ine kacinja, koma Mulungu watate ali naine. \v 6 Muziba kuti na mphavu zanga zonse na nkhala nisebenzera batate banu.

1
31/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Batate banu baninama na kucinja malipilo yanga kali 10, koma Mulungu sana muvomeka kucita coipa. \v 8 Ngati anakamba kuti, nyama za manthongo ndiye malipiro yako, 'ndipo zonse nyama zinabala zamanthongo, ngati akamba kuti, zamizela zizakhala malipiro yako, ' ndipo nyama zonse zinabala zamizera. \v 9 Cifukwa cake Mulungu anatenga nyama za batate banu na ni pasa.

1
31/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Ndipo pa nthawi yobala, ninaona muciloto mbuzi zimuna zinali kukwra nyama. Mbuzi zimuna zinali namizera, namanthongo na mitundu yosiyana siyana. \v 11 Mungelo wa Mulungu anakamba naine muciloto, 'Yakobo,' nakamba,' 'Ine nilipano.'

1
31/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Anakamba, 'Nyamula menso yaku ndipo uone mbuzi zonse zimuna zikwerana na nyama. Zinamizela, Manthongo, na mitundu yosiyanasiyana, cifukwa nabona vonse vamene Labani acita kuli iwe. \v 13 Ndine Mulungu wa Betele, kwamene Mathira mafuta pamwala, kwamene unalumbilila kuli ine. Manje nyamuka ucoke m,malo yano ndi kubwelera kumalo kwamene unabadwira.'"

1
31/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Rakele ndi Leya anayankha ndi ku kamba nayeve, kodi kulibe gao na vosalira vanthu munyuma yatate? \v 15 Kodi sitisungiwa na yeve monga ba lendo? cifukwa atigulisa na kusilizilatu kuononga ndala zathu. \v 16 Pa cuma conse camene Mulungu acosaka kuli batate bthu cankuala cathu na bana bathu. Manje, vilivonse vamene Mulungu akamba, cita."

1
31/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Ndipo Yakobo ananyamuka noika bana bake bamuna na bazikazi bake pa ma bulu. \v 18 Anaika zobeta zake pa songolo pake, pamozi nakatundu wake bonse, kuikilapo nanyama za mene anakhala nazo mu paddani Aramu. Ndipo anakonzekera kuyenda kuli Isaki tate wake mumalo yao ya Kanaani.

1
31/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Pamene Labani anayenda kukasenga nkhosa zake, Rakele anaba tumilungu twa munyuma ya batate bake. \v 20 Yakobo ana namanso Labani wa ku Aramean, po samu uza ati ayenda. \v 21 Ndipo anathaba na vonse enze navo na kudusa pa mumana, ndipo anayendela ku phili yaziko ku Giliyadi.

1
31/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Pasiku ya citatu Labani ana uziwa kuti Yakobo anathaba. \v 23 Ndipo anatenga abale ake ndi kumupisha kwa ulendo wamasiku seveni. Anamupeza pa phiri ya ziko ya ku Giliyadi.

1
31/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Ndipo Mulungu anabwera kwa Labala mu Aramean muciloto naku mu uza kuti, "Nkhala ocenjera kuti osakambe voipa olo vabwino kuli Yakobo. \v 25 "Labani anapitilila Yakobo. Ndipo Yakobo anamanga hema yake mupili yaziko. Labani naye anakhala paja mba bale bake mupili ya Giliyadi.

1
31/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 Ndipo Labani anakamba kuli Yakobo, wacita cani, kuti unani nama nakunyamula bana banga bakazi monga ba kaida ba nkhondo? \v 27 Cifukwa nicani unathaba mwacisinsi na kuninama ndiponso sunani uze ine? Asembe nina kupelekeza nakusangalala na nyimbo, ndi lingaka ndi coliza. \v 28 Sunandi vomekeze ine ku mpsompsona bana banga bakazi na bamuna, manje wacita vopusa.

1
31/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Vili mu mphavu zanga kukucita voipa, koma Mulungu waba tate bako anakamba usiku wasila ndipo anati, 'Khala wocenjela, kuti osakambe kuli Yakobo voipa na vabwino.' \v 30 Manje wayenda cifukwa wenze kufuna maningi kubwelela kunyumba ya batate bako. Nanga nichani camene unabela milungu yanga?"

1
31/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 Yakobo anayankha nanena kwa Labani, "Chifukwa ninayopa nakuganiza kuti muzapoka bana banu bakazi mwampavu ndaba sinilaile. \v 32 Alionse wamene aba milungu yanu saza pitiliza kukhala na moyo. Pamenso ya ba bale bathu, ona cili conse cili naise ngati nichanu mucitenge. "Cifukwa Yakobo sanazibe kuti Rakele ndiye anaba.

1
31/33.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 33 Labani anangena muhema ya Yakobo, na muhema ya Leya, ndiponso muhema ya banchito babili, koma sanaba peza. Anocoka muhema ya Leya na ku ngena muhema ya Rakele.

1
31/34.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 34 Ndipo Rakele anali anatenga milungu zamunyumba, anaviika pa conkhalila caca ngamila, ndi kunkhalapo. Labani anasakila muhema yonse, koma sana vipeza. \v 35 Anakamba kuli atate bake, "Osakalipa, mbuye wanga, kuti siningamilile pamenso pano, cifukwwwa nili panthawi ya kumwezi. "Ndipo anasakila koma sana peza milungu za munyumaba mwake.

1
31/36.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 36 Yakobo anakalipa naku kangana na Labani. Anakamba kwa iye, "Kodi mulandu wanga ndiwa bwanji?Cimo yanga niya bwanji, kuti muzingo kuni konka konka? \v 37 Popeza mwa sukila ponge pali katundu yanga. Nichani came mwapeza pavinthu vonse va munyumba yanu? Vileteni apa pali abale athu, kuti ba weruzu pakati ka ife.

1
31/38.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 38 Kwazakatwenti na nkhala naimwe. Nkhosa zanu nambuzi zikazi sizina kangangepo kubala, olo kapena kudyapo pa vo beta vako. \v 39 Vina vina ng,ambiwa na vilombo sinina vilete kuli iwe, koma, ndine ninalipila pava mene vinasowa. Nthawi zonse mumanindi pilisa pali nyama yadoba, loko yabewa usiku olo muzuba. \v 40 Ndipo nenzeko, musiku zuba inani shoka, mame ya usiku ndipo sinina gone usiku.

1
31/41.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 41 Izi zake twenti nankhala munyumba yako, nina kusebenzela iwe zaka fotini cifukwa ca bana bako babili bakazi, nazaka sikisi vobeta vako. Mwacinja malipilo kali teni. \v 42 Pokhapo Mulungu wa batate banga, Mulungu wa Abrahamu ndi iye wamene kaki ayopa, anali na ine, zo ona mwenze kuti niyende popanda vilivonse mu manja mwanga. Mulungu ayangana kuvutika kwanga na mwamene nenze kusebenzera maningi, ndipo anaku kalipila busiku wayenda."

1
31/43.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 43 Labani anayankha na ku kamba kuli Yakobo, "Akazi aba ndiye bana banga bakazi, bazukulu niba zukulu bangaa, navobeta ni vobeta vanga. vonse vamene uona nivanga. Koma nichani lelo ninga cite kuli aba banga bakazi kapene bana bao bamene bana bala? \v 44 Manje apa, tiye tipange cipangano, iwe naine,ndipo ndiye ciza nkhala kamboni pakati ka iwe na ine."

1
31/45.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 45 Ndipo Yakobo anatenga mwala nakuika pamwamba pa pila. \v 46 Yakobo anakamba kuli babale bake, "Ikani miyala pamozi," ndipo banatenga miyala nakuzi bunjika. Ndipo banadyela pamwamba. \v 47 Labani ana itanapo Jegara saha Duthu, koma Yakobo anaitanapo Gilayadi.

1
31/48.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 48 Labani anakamba, izi miyala ni kamboni pakati kaiwe naine, lelo "Cifukwa cake zina yake baitanapo Giliyadi. \v 49 Paitaniwanso mizipa cifukwa Labani anakamba, Leka Yehova ayangane pakati kaiwe na ine, pamene tisiyana wina na muzake. \v 50 Ngati suzasunga bana banga bakazi bwino, olo uzatenga bakazi bena pambali ya bana banga bakazi, loko palibe wina ali naise, ona, Mulungu ni kamboni pakati kaiwe na ine."

1
31/51.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 51 Labani anakamba kuli Yakobo, " Yangana pamwamba, ndipo ona pa pila, yamene naika pakati kaiwe naine. \v 52 Iyi nthutu ndiye kamboni, na pila ni kamboni kuti sinaza jumpa iyi nthutu kubwera kuli iwe, ndipo na iwe suza jumpa iyi nthutu ku bwela kuli ine, kucita voipa. \v 53 Leka Mulungu wa Abrahamu, na Mulungu wa Nahor, na milungu za ba tate bao, ziweruza pakati kathu." Ndipo Yakobo analapa pakuyopa batate bake Isaki.

1
31/54.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 54 Yakobo ana peleka nsembe pa phiri nakuitana abale bake kuti bazadye cakudya. Ba nadya na kunkhala busiku bonse pamwamba pa lupili. \v 55 mumawa, Labani anauka, naku myompyona bazulu bake na bana bake bakazi na kubadalisa. Pamene Labani anacokapo nakubwelera kunyumba.

1
42/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 42 \v 1 Ndipo Yakobo anaona kuti munali vakudya mu Egipito. Anakamba kuli bana bake bamuna. Cifukwa nichani muyang'ana yang'ana? \v 2 Anakamba, onani apa, namvera kuti kuli vakudya mu Egipito, Yendakoni kuti mukati gulile kuti tinkhale namoyo tisamwalile. \v 3 Abale bake ba Yosefe bali banayenda kugula vakudya ku Egipito. \v 4 Koma Yakobo sana tume benjamini, mubale wake wa yosefe, pamozi na bale bale popeza anakamba kuti, "Niyopa kuti voipa vingacitike pali yeve.

1
42/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Bana ba Israyeli banabwera kugura pakati kabaja banabwera, cifuka njala inali mu ziko ya Kanani. \v 6 Ndipo Yosefe anali bolamulila ziko. Ndipo anali kugulisa kubanthu bonse ba muziko. Abale bake ba Yosefe banafika nakubelama pansi na nkhope zao pansi.

1
42/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Yosefe anaona babele bake nakubaziba ana zibisi kuli beve naku kamba nabo mo limba anakamba nao, mwacokela kuti? Banakamba kuli tacokela ku Kanani kubwela kugula vo kudya. \v 8 Yosefe anabaziba ba bale bake, koma beve sibana muzibe.

1
42/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Ndipo Yosefe anakumbuka viloto vamene analota pali beve, anakamba nabeve kuti, ndimeneo oipa mwabwela kuona mbali zamene zilibe citezo mu ziko. \v 10 " Anakamba kuli yeve kuti, awe mbuye wanga. Ba kapolo bako babwla kugula vakudya. \v 11 Ndise bana bamunthu umozi tonse, ndife banthu bazoona, bakapolo bako si banthu oipa.

1
42/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Anakamaba nao kuti, "Awe, mwabwela kuona malo mulibe citeyezo mu ziko \v 13 Bana kamba kuti, "Ife akapolo bako tili abale tyovu, bana bamunthu umozi muziko ya kenani. Ona, mufuna maningi lelo ali nabatate bathu na mubale wathu umozi salimoyo."

1
42/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Yosefe anababuza kuti, "Ndiye vamene naku uzani. ndimwe oipa. \v 15 Pali ici muza yesewa na moyo wa falabo, simuzacoka pario, koma cabe ngati mubale wanu mung'onu abwere kuno. \v 16 Tmani umozi mumusiye akatenge mubale wanu. Muzasala mundende, kuti mau yanu yayesewe. Kuona ngati muli cazo ona muli imwe. Ngati siivo, pa moyo wa Falao ndimwe oipa zo ona. \v 17 Anaika bonse mundende musiku yatatu.

1
42/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Yosefe anakamba nabeve pasiku yacitatu, " Citani ici kuti mukhale namoyo, Popeza niyopa Mulungu. \v 19 Ngati ndimwe bamuna bazo ona, lekani umozi wa abale wanu akhale mundende iyi, koma imwe mu yende, nyamulani vokodya vanjala ya manyumba yanu. \v 20 Bwelesani mufana wanu kuti mau yanu ya simikiziwe ndipo simuza mwalila." Ndio banacita zimezo

1
42/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Banakambisana wina na muzake, " tinachimwila mubale wathu pakuti tina ona ,kutika kwa moyo wake pamene ana papata kuli ife pamene. anati pempha ndipo sitinamvela, cifukwa caici mavuto yatifikila. cifukwa caici mvuto yatikila. \v 22 Rubene anabayankha, "KOdi sina kuuzane, Osamucimwila munyamata! Koma sina mvele? Manje onani, magazi yake ya funika kwa ife."

1
42/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Sabanazibe kuti Yosefe anabamwesesa, cifukwa panali omasulila pakati kao. \v 24 Anacoka pali beve ndipo analila. Ana bwelela kuli beve nokamba nao. Anatenga simiyoni nakumu manga menso yao. \v 25 Yosefe ana lamulila ba nchito bake kuti ba zuze machola na vakudya, ndikuika ndalama za munthu alibonse mucola cake, ndi ku bapasa vose vofunika paulendo. zinacitika.

1
42/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 Abale anasenzesa Abulu ao vakudyandi kuyambapo. \v 27 Pamene umozi anasegula saka kuti apase bulu zakudya mu malo yopumulila, ana ona ndalama zake. Taonani zinali muku segula kwa thumba yake. \v 28 Anakamba kuli abale ake, " Ndalama zanga za bwezewamo, zioneni, zili mutumba yanga, "Mitima yanamila anapindamuka monjemela kuyanganana wina na mzake, kukamba kuti, "Nicani ici camene Mulungu acita kuli ise?"

1
42/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Anayenda kwa Yakobo, tate wo muziko ya Kanani ndi kumu uza vonse vinaba citikila. Banakamba kuti. \v 30 Munthu, mbuye waziko, an anakamba, naise moka lipo nakuti ona monga ndise oipa muziko. \v 31 Takamba kuli yeve, ndife bamuna bazona, sindife boipa. \v 32 Tili abale tyovu, bana ba atate bathu, umozi salimoyo, ndipo ndipo mung'ona lelo ati na batate muziko ya Kenani.

1
42/33.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 33 Munthoyo, mwine ziko, anakamba naise, kupitila muli ici nizaziba kuti ndimwe amuna bazo ona. Siyani mubale wanu umozi naine,, tengani vakudya ya njala ku manyumba yanu, ndipo yambaponi. \v 34 Bwelesani mufana wanu maningi kuli ine. Ndipo nizaziba kuti sindimwe oipa, koma kuti ndimwe bamuna bazoona, Pamenepo ndizatulusa mubale wanu, ndipo muzagulisa muziko."

1
42/35.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 35 Vinacita pamene anasegula matumba yao kuti, taonani, thumba yalionse munali siliva. Pamene beve naba tate bao banaona mutumba ya siliva, banayopa. \v 36 Yakobo tate wao anakamba kuli beve, "Mwanitengela bana banga, Yosefe salimoyo, Simioni naye ayenda, ndipo mufuna kutenga Benjamini. Vonse ivi vinthu vaninyamukila ine."

1
42/37.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 37 Rubene anakamba naba tate bake, kuti, mungapaye bana banga babili ngati siniza bwelesa Benjamini kuli imwe, muakeni mumanja yanga, ndipo ndizaleta kuli imwe futi." \v 38 Yakobo anati, "Mwana wanga mwamuna sazayenda naiwe, popeza mubale wake anafa ndipo anasala yeka. Ngati voipa vizabwela pali yeve munjira yamene muyendamo, ndipo muzaleta imvi zanga ndicisoni kumanda.

1
42/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 42

View File

@ -1,5 +1,5 @@
{
"package_version": 6,
"package_version": 7,
"format": "usfm",
"generator": {
"name": "ts-desktop",
@ -103,6 +103,16 @@
"05-28",
"05-30",
"05-32",
"08-title",
"08-01",
"08-04",
"08-06",
"08-08",
"08-10",
"08-13",
"08-15",
"08-18",
"08-20",
"09-title",
"09-01",
"09-03",
@ -210,7 +220,54 @@
"25-27",
"25-29",
"25-31",
"27-title",
"27-01",
"27-03",
"27-05",
"27-08",
"27-11",
"27-13",
"27-15",
"27-18",
"27-20",
"27-22",
"27-24",
"27-26",
"27-28",
"27-29",
"27-30",
"27-32",
"27-34",
"27-36",
"27-38",
"27-39",
"27-41",
"27-43",
"27-46",
"31-title",
"31-01",
"31-04",
"31-07",
"31-10",
"31-12",
"31-14",
"31-17",
"31-19",
"31-22",
"31-24",
"31-26",
"31-29",
"31-31",
"31-33",
"31-34",
"31-36",
"31-38",
"31-41",
"31-43",
"31-45",
"31-48",
"31-51",
"31-54",
"33-title",
"33-01",
"33-04",
@ -252,6 +309,21 @@
"40-16",
"40-18",
"40-20",
"42-title",
"42-01",
"42-05",
"42-07",
"42-09",
"42-12",
"42-14",
"42-18",
"42-21",
"42-23",
"42-26",
"42-29",
"42-33",
"42-35",
"42-37",
"43-title",
"43-01",
"43-03",