nya-x-nyanja_gen_text_reg/04/25.txt

1 line
342 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 25 Adamu ana Ziba mukadzi wake nafuti, ndipo mukadzi wake abala mwana wina mwamuna. Anamu pasa zina yakuti Seti nakukamba kuti, "Mulungu anipasa mwana mwamuna winangu pamalo ya Abelo, chifukwa Kaini anamu paya." \v 26 Mwana mwamuna anabadwa kuli Seti amanupasa dzina yakuti Enosi. Panthawi iyo banthu banayamba kuyitana pa dzina ya Yehova.