nya-x-nyanja_gen_text_reg/45/24.txt

1 line
343 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 24 Ndipo anabatuma ba bale bake kuti ba yambepo. Anabauza kuti, " Muone kuti musayambane munjila." \v 25 Bana choka mu Igupto nakubwela ku ziko la Kanani, kwa Yakobo tate wabo. \v 26 Banamu uza kuti, " Yosefe akali moyo, ndipo wamene alamulila mu ziko yonse ya Igupto." Mutima wake unadabwa,, chifukwa sana kulupilile vamene bana mu uza.