nya-x-nyanja_gen_text_reg/29/11.txt

1 line
196 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 11 Yakobo ana pyopyonta Recho nakulila mo kuwa. Yakobo anauza Recho, kuti enve anali bululu wa batate bake, anali mwana wa Rabeka. \v 12 Pamene apo enve anatmnaga na kuyenda ku'uza batate bake.