\v 7 Zina chitika ku choka apa kuti mukazi wa bwana wake anamu kumbwila Yosefe no kamba, " Gona na ine." \v 8 Koma anakana ku gona naba kazi ba abwana bake, " Ona, bwan wanga sama ikako nzelu ku vonse nichita mu nyumba yabo, anani ika ku langanila vonse vintu vabo. \v 9 Kulibe mwamukulu mu nyumba muna pali ine sana bisa kantu kuli ine koma iwe, chifukwa ndiwe mukazi wake. Ninga chite bwanji zo ipa izi naku chimwila Mulungu?"