Yahova Mulungu anaitana mwamuna nakumufunsa kuti, " Uli kuti?" \v 10 Mwamuna anayankha kuti, " Nakumverari mu munda, nenze na mantha, ndaba nenze cinthako. Nenze nabisama." \v 11 Mulungu anakamba, " Nindani akuuza kuti wenze cinthako? Kodi wadya mumtengo