\v 14 Yakobo anaika mwala ukulu pamalo pamene Mulungu anali ku kamba naye. Pila ya mwala. Anafilapo chakumwa kunkala ngati nsembe na mafuta. \v 15 Yakobo anaitana malo yamene Mulungu analikukamba naye, bethel.