nya-x-nyanja_gen_text_reg/31/29.txt

1 line
297 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 29 Vili mu mphavu zanga kukucita voipa, koma Mulungu waba tate bako anakamba usiku wasila ndipo anati, 'Khala wocenjela, kuti osakambe kuli Yakobo voipa na vabwino.' \v 30 Manje wayenda cifukwa wenze kufuna maningi kubwelela kunyumba ya batate bako. Nanga nichani camene unabela milungu yanga?"