2020-11-23 08:34:46 +00:00
|
|
|
\v 8 Kaini ana kamba na Abelo mu bale wake. Zinachika kuti pamene banali mu minda Kaini anaukila mubale wake naku mupaya. \v 9 Ndipo Yehova anafunsa Kaini, "Alikuti Abelo nubale wako?" Anakamba, "Sinniziba. Nanga ndine malonda wake?"
|