nya-x-nyanja_gen_text_reg/20/10.txt

1 line
355 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 10 Abimeleki anakamba kuti kwa Abrahamu, " Unaona cani kuti ucite ici cinthu?" \v 11 Abrahamu anakamba kuti, " Cifukwa ninaganiza, ' zoona mulibe kuyopa mulungu mu malo muno ndipo bazanipaya cifukwa ca mkazi wanga.' \v 12 Pakuti, zoona ninabadwa naye, ni mwana mkazi wa batate banga, koma osati mwana mkazi wa amai banga; ndipo anankhala mkazi wanga.