\v 15 Esau anakamba, " Lekani nikusiyileni amuna banga amene bali na ine" Koma Yakobo anayankha, " Ciani mzacitila izo? Lekani nipeze mwayi pamanso ya bwana wanga." \v 16 Ndipo Esau pa siku ija anayambapo ulendo wake kupita ku Seiri. \v 17 Yakobo anayenda ku sokoti, kukazimangila iye mwine nyumba na makolo ya zibeto zake. Ndipo zina la malo ndi Sokoti.