\v 4 Tili nacho chikulupililo mwa Ambuye pa imwe, kuti muzachita koma futi muzapitiliza kuchita vintu vamene tikuuzani. \v 5 Lekani Ambuye basogolele mitima zanu mu chikondi cha Mulungu na mukulimbikila mwa Kristu.